The team at Kodi Fire IPTV strongly suggests that you use a VPN at all times. Be it for browsing, watching Kodi, watching IPTV or anything else – the one that we recommend is Quad VPN. They provide you with very fast speeds, while keeping you protected. They can also unblock most streaming sites in the US and UK!! Grab your own Quad VPN and regain your online privacy now!
muzaona mukazakwatiwa , ndichisomo kupeza mkazi yemwe ali ndi china chonse mwa iye komano in lfe palibe yemwe ali okwanila aliyense ngoperewela somehow , zimangofunika kuziwa nzakoyo amakonda kumvelana basi nothing else , mwamuna or mkazi amatuluka kunja ngati sedrvice ya munthu winayo siliboo zimafunika osachita pretend koma be genuine
muzaona mukazakwatiwa , ndichisomo kupeza mkazi yemwe ali ndi china chonse mwa iye komano in lfe palibe yemwe ali okwanila aliyense ngoperewela somehow , zimangofunika kuziwa nzakoyo amakonda kumvelana basi nothing else , mwamuna or mkazi amatuluka kunja ngati sedrvice ya munthu winayo siliboo zimafunika osachita pretend koma be genuine
Eya timafuna kusinthila
Vuto ndiloti azibambo ambirife timakwatira komano sitikuziwa chenicheni chifukwa chomwe takwatilira.
Atadipatsa style ya sakwanya ndindingapite eee I we ineneyo ngat m'pela natukane jomba
Uwafunse azimayi anzanuwo
Kkkkkkkkk
Going out for what, if everything is ok, then it can not happen.
Iweyo mamunako sapita kunja?
Ay pafunika kuperekeratu
is one woman enough?….my answer is No.
Poverty is what keeps a man at home.
Sungapite akukunyengetsa bwino
Ife tilibwino kunoku ku Zambia, amai mwafusako, bwino, ta amuna tili siyana siyana, ana amuna, anakula kukhala nachizolowezi,, chokha ndi azikazi ambili mbili, koma mwanazi si musiyanabe ai. Koma, musiyana kasamalilo kakuthupi kwanu, ena amadyako twina kuti azikazi mukhale okoma koma ena yai tele, somwamuna akayenda kwina akalawa apambanisa namukazi wake, ndicho chifukwa Kwambili icho tili nacho amuna zikomo. Ndine banda esited, Kuno kuzambia kulundazi chief zumwanda.
Tipitabe, nagasi timafuna titapange benchmarking ndiyena
Amuna kusiyana Koma ine ndiye sindingapite kunja
Palibe kadzi yemwe angakwanise zifuna zamamuna.kms akadzi inu mumaderel kwambiri mumayakhula zamwano mumati ine ndikhalire zimenezo zongogonanazo ngt zili zimenezo kapezen wina. Ndye ife azibambo popewa zimenezo ndichifukwa timapanga zibwezi zaseli.
Sitingamapite kunja tizionetsetsa kuti mkaz asatalikire yakho ndilakuti sitingapitenso kunja.
Muzibambo ndiwosiyana ndi mzimai
Chifukwa ndikovuta muzibambo kukwerA azikazi atatu anai nthwawi imodzi
Pamene mkazi ngakare 20 angajekere nthwawi imodzi
Ndichimapangitsa ndikusilira basi kufuna kuona mataipi taipi
Komanso xhimapangitsanso pariwena saatha kupilira mwina mkazi ariku períod kuti aembekeze saatha wenasso azikazi amaonjeza mwina pamwezi kawiri kusamba
Azimayi ngambiri,azibambo ngochepa,tsona kupanda kupita kunja ena zimayi osowa mabanja amadandaula
Azibambo ndi anthu osavuta koma aximayi ena mbola
Aise zokuluwika pano ai simwabwela nayo nkhani imeneyi,ndi inu?lero tikuudzani chifukwa ambiliwa akulephela ku nena zoona choyambilila mwamuna yemwe alibe yesu.ndi omwe amachita zimenezi.kachiwili,chilichonse ndi mwamuna ayenela kuphudzitsa kazacheyo,kaphikidwe.kachitatu,akazi asiye kubelekesedwa ndi azamba,akakhala odwala azipita ku chipatala.Chifukwa kuchipatala amakuudzani muzikathila mafuta ndiyo zanuzi mutabvinikila pomwe kwa azamba amangoti thilani chele basi zathela popo mamuna abwele adye zisakhala bwinotu Kkkkkkk wakulu akudziwa kuti ndikuthandaudza chiyani iyaa
Sindingasiye, ngati za kukwana uona kuti utani, ngati ndukusamalila you don't dare to tell me what do or not to do,
Nanga azikazinu mwamuna atamakupatsani zonse mungamapitenso kwina?