ZaKUCHIPINDA, Kodi azibambo mungasinthe zofunsila kwina mkazi atamapanga zomwe inu mukufuna ???




[matched_content]



The team at Kodi Fire IPTV strongly suggests that you use a VPN at all times.
Be it for browsing, watching Kodi, watching IPTV or anything else – the one that we recommend is Quad VPN. They provide you with very fast speeds, while keeping you protected. They can also unblock most streaming sites in the US and UK!!
Grab your own Quad VPN and regain your online privacy now!

22 COMMENTS

  1. muzaona mukazakwatiwa , ndichisomo kupeza mkazi yemwe ali ndi china chonse mwa iye komano in lfe palibe yemwe ali okwanila aliyense ngoperewela somehow , zimangofunika kuziwa nzakoyo amakonda kumvelana basi nothing else , mwamuna or mkazi amatuluka kunja ngati sedrvice ya munthu winayo siliboo zimafunika osachita pretend koma be genuine

  2. Ife tilibwino kunoku ku Zambia, amai mwafusako, bwino, ta amuna tili siyana siyana, ana amuna, anakula kukhala nachizolowezi,, chokha ndi azikazi ambili mbili, koma mwanazi si musiyanabe ai. Koma, musiyana kasamalilo kakuthupi kwanu, ena amadyako twina kuti azikazi mukhale okoma koma ena yai tele, somwamuna akayenda kwina akalawa apambanisa namukazi wake, ndicho chifukwa Kwambili icho tili nacho amuna zikomo. Ndine banda esited, Kuno kuzambia kulundazi chief zumwanda.

  3. Muzibambo ndiwosiyana ndi mzimai
    Chifukwa ndikovuta muzibambo kukwerA azikazi atatu anai nthwawi imodzi
    Pamene mkazi ngakare 20 angajekere nthwawi imodzi
    Ndichimapangitsa ndikusilira basi kufuna kuona mataipi taipi
    Komanso xhimapangitsanso pariwena saatha kupilira mwina mkazi ariku períod kuti aembekeze saatha wenasso azikazi amaonjeza mwina pamwezi kawiri kusamba

  4. Aise zokuluwika pano ai simwabwela nayo nkhani imeneyi,ndi inu?lero tikuudzani chifukwa ambiliwa akulephela ku nena zoona choyambilila mwamuna yemwe alibe yesu.ndi omwe amachita zimenezi.kachiwili,chilichonse ndi mwamuna ayenela kuphudzitsa kazacheyo,kaphikidwe.kachitatu,akazi asiye kubelekesedwa ndi azamba,akakhala odwala azipita ku chipatala.Chifukwa kuchipatala amakuudzani muzikathila mafuta ndiyo zanuzi mutabvinikila pomwe kwa azamba amangoti thilani chele basi zathela popo mamuna abwele adye zisakhala bwinotu Kkkkkkk wakulu akudziwa kuti ndikuthandaudza chiyani iyaa