The team at Kodi Fire IPTV strongly suggests that you use a VPN at all times.
Be it for browsing, watching Kodi, watching IPTV or anything else – the one that we recommend is Hidden Router. They provide you with very fast speeds, that can reach over 400Mbps, and their VPN service is as low as $6 per month (when paid for 2 years)!
Grab your own Hidden Router and regain your online privacy now!

23 COMMENTS

  1. In 2020 Nnadutsa mnyengo yowawitsa, ulendo wanga wa mimba unali owawa mpakana kubeleka, , koma inali nyengo yowawitsa😭😭😭😭 after all these sufferings mwangayo nkudzamwaliraso ali ndi miezi iwiri, nde mpakana pano ndimadzifunsabe mafunso kuti kodi Yesu Amasamaladi???

  2. Ndine mbon kut Yesu amasamala Amen amen kuyambira 2015 kuzafik 2020 mmmm moyo umawawa kwambir ndimagonera jolly jus ndiana anga ndasi limodzi kunyemana kkkk kma Yesu ameneyu zomwe anandichitira dziko silikumvetsa ,pano zakudya sinkhan azibale anga pano akudalira ine Hahaha Hahaha ,ngt mlipo ena mlindifunso ngt ili ayi ndingt Ambuye akuonekeren kut nanu mkhale ndiyankho Amen mdalitsike mama.